Oweruza 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anasonkhana eni ace onse a ku Sekemu, ndi nyumba yonse ya Milo, namuka namlonga Abimeleki ufumu pa thundu wa coimiritsa ciri m'Sekemu.

Oweruza 9

Oweruza 9:1-14