Oweruza 9:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Natuma mithenga kwa Abimeleki monyenga nati, Taonani Gaala ndi abale ace afika ku Sekemu; ndipo taonani, akupandukitsirani mudzi.

Oweruza 9

Oweruza 9:23-39