Oweruza 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo abale a amace anamnenera mau awa onse m'makutu a eni ace onse a Sekemu; ndi mitima yao inalunjika kutsata Abimeleki; pakuti anati, Ndiye mbale wathu.

Oweruza 9

Oweruza 9:1-10