Oweruza 8:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Gideoni anati, Cifukwa cace, Yehova akapereka Zeba ndi Tsalimuna m'dzanja langa, ndidzapuntha nyama yanu ndi minga ya m'cipululu ndi mitungwi.

Oweruza 8

Oweruza 8:1-12