Oweruza 8:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena kwa amuna a ku Sukoti, Mupatsetu anthu awa akunditsata mitanda yamkate; pakuti atopa, ndipo ndirikulondola Zeba ndi Tsalimuna mafumu a Midyani.

Oweruza 8

Oweruza 8:4-8