Oweruza 8:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anthu a Israyeli anati kwa Gideoni, Mutilamulire ndi inu, ndi mwana wanu, ndi mdzukulu wanu, pakuti mwatipulumutsa m'dzanja la Amidyani.

Oweruza 8

Oweruza 8:13-30