Oweruza 8:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anati kwa Zeba ndi Tsalimuna, Amunawo munawapha ku Tabori anali otani? Iwo nayankha, Monga iwe momwemo iwowa; yense wakunga mwana wa mfumu.

Oweruza 8

Oweruza 8:17-26