Oweruza 8:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Zeba ndi Tsalimuna anathawa; koma anawatsata, nagwira mafumu awiri a Midyani Zeba ndi Tsalimuna, nanjenjemeretsa khamu lonse.

Oweruza 8

Oweruza 8:3-19