Oweruza 7:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anthu anatenga kamba m'dzanja lao, ndi malipenga ao; ndipo anauza amuna onse a Israyeli amuke, yense kuhema kwace; koma anaimika amuna mazana atatuwo; ndipo misasa ya Midyani inali kunsi kwace m'cigwa.

Oweruza 7

Oweruza 7:1-14