Oweruza 6:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anakwera nazo zoweta zao ndi mahema ao, analowa ngati dzombe kucuruka kwao; iwowa ndi ngamila zao zomwe nzosawerengeka; ndipo analowa m'dziko kuliononga.

Oweruza 6

Oweruza 6:1-7