Oweruza 6:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

taonani, ndidzaika cikopa ca ubweya popunthira tirigu; pakakhala mame pacikopa pokha, ndi panthaka ponse pouma, pamenepo ndidzadziwa kuti mudzapulumutsa Israyeli ndi dzanja langa monga mwanena.

Oweruza 6

Oweruza 6:35-40