Oweruza 6:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mzimu wa Yehova unabvana Gideoni; naomba lipenga iye, ndi a banja la Abieziri analalikidwa kumtsata iye.

Oweruza 6

Oweruza 6:29-40