Oweruza 6:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace anamucha tsiku lija Yerubaala, ndi kuti, Amnenece mlandu Baala popeza anamgamulira guwa lace la nsembe.

Oweruza 6

Oweruza 6:22-39