Oweruza 6:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Gideoni anaona kuti ndiye mthenga wa Yehova, nati Gideoni, Tsoka ine, Yehova Mulungu! popeza ndaona mthenga wa Yehova maso ndi maso.

Oweruza 6

Oweruza 6:18-24