Oweruza 6:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Gideoni analowa, nakonza kambuzi ndi mikate yopanda cotupitsa ya muyeso wa ufa; nyamayi anaiika m'licero, ndi msuzi anauthira mumbale, naturuka nazo kwa iye ali patsinde pa thundu, nazipereka.

Oweruza 6

Oweruza 6:12-28