Oweruza 5:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova, muja mudaturuka m'Seiri,Muja mudayenda kucokera ku thengo la Edomu,Dziko linanjenjemera, thambo lomwe linakha,Inde mitambo inakha madzi.

Oweruza 5

Oweruza 5:1-8