Oweruza 5:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dzanja lace analitambasulira kuciciri,Ndi dzanja lace lamanja ku nyundo ya anchito,Nakhomera Sisera, nakantha mutu wace,Inde, anaphwanya napyoza m'litsipa mwace.

Oweruza 5

Oweruza 5:23-31