Oweruza 4:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Kumuka ndidzamuka nawe, koma ulendo umukawo, sudzacita nao ulemu; pakuti: Yehova adzagulitsa Sisera m'dzanja la mkazi, Motero Debora anauka namuka ndi Baraki ku Kedesi.

Oweruza 4

Oweruza 4:1-13