Oweruza 4:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sisera ananena naye, Taima pakhomo pa hema, ndipo kudzali, akadza munthu, akakufunsa akati, Pali munthu pano kodi? Uziti, Palibe.

Oweruza 4

Oweruza 4:10-23