Oweruza 4:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Sisera anasonkhanitsa magareta ace onse ndiwo magareta mazana asanu ndi anai acitsulo, ndi anthu onse okhala naye, kuyambira Haroseti wa amitundu mpaka mtsinje wa Kisoni.

Oweruza 4

Oweruza 4:4-15