Oweruza 4:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Heberi Mkeni anadzisiyanitsa ndi Akeni, ndi ana a Hobabu mlamu wace wa Mose, namanga mahema ace mpaka thundu wa m'Zaananimu, ndiwo wa ku Kedesi.

Oweruza 4

Oweruza 4:6-19