Oweruza 3:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ehudi anadzisulira lupanga lakuthwa konse konse utali wace mkono; nalimangirira pansi pa zobvala zace pa ncafu ya kulamanja.

Oweruza 3

Oweruza 3:15-24