Oweruza 21:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iwo, Kodi pali lina la mapfuko a Israyeli losakwera kudza kwa Yehova ku Mizipa? Ndipo taonani, kucokera ku Yabesi-gileadi sanadza mmodzi kumisasa, kumsonkhano.

Oweruza 21

Oweruza 21:1-13