Oweruza 21:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anacokako nthawi ija yense kumka ku pfuko lace, ndi banja lace, naturukako yense kumka ku colowa cace.

Oweruza 21

Oweruza 21:15-25