Oweruza 21:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu anadza ku Beteli, nakhala pansi pomwepo pamaso pa Mulungu mpaka madzulo; nakweza mau ao ndi kulira misozi yambiri.

Oweruza 21

Oweruza 21:1-6