Oweruza 21:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Natiiwo, Taonani, pali madyerero a Yehova caka ndi caka ku Silo, ndiko kumpoto kwa Beteli, kum'mawa kwa mseu wokwera kucokera ku Beteli kumka ku Sekemu, ndi kumwela kwa Lebona.

Oweruza 21

Oweruza 21:18-25