Oweruza 21:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapeza mwa anthu a Yabesi-gileadi anamwali mazana anai osadziwa mwamuna mogona naye; nabwera nao kumisasa ku Silo, ndiwo a m'dziko la Kanani.

Oweruza 21

Oweruza 21:7-21