Oweruza 20:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nabwerera iwo pamaso pa amuna a Israyeli kumka njira ya cipululu; koma nkhondo inawaloodetsa; ndi aja oturuka m'mudzi anawaononga pakati pao.

Oweruza 20

Oweruza 20:41-48