Oweruza 20:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Benjamini anawaturukira ku Gibeya m'mawa mwace, naononganso a ana a Israyeli amuna zikwi khumi ndi zisanu ndi zitatu kuwagoneka pansi; ndiwo onse osolola lupanga.

Oweruza 20

Oweruza 20:18-27