Oweruza 20:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nauka ana a Israyeli, nakwera kumka ku Beteli, nafunsira kwa Mulungu, nati, Ayambe ndani kutikwerera pa ana a Benjamini? Ndipo Yehova anati, Ayambe ndi Yuda.

Oweruza 20

Oweruza 20:17-26