Oweruza 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cacenso ndinati, Sindidzawapitikitsa kuwacotsa pamaso panu; koma adzakhala ngati minga m'nthiti zanu, ndi milungu yao idzakhalira inu msampha.

Oweruza 2

Oweruza 2:1-4