Oweruza 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Israyeli, ndipo anawapereka m'manja a ofunkha kuti awafunkhe; nawagulitsa m'dzanja la adani ao akuwazungulira osakhozanso iwowo kuima pamaso pa adani ao.

Oweruza 2

Oweruza 2:13-23