Oweruza 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nasiya Yehova Mulungu wa makolo ao, amene adawaturutsa m'dziko la Aigupto, natsata milungu yina, milungu ya mitundu ya anthu okhala pozungulira pao, naigwadira; nautsa mkwiyo wa Yehova.

Oweruza 2

Oweruza 2:7-14