Oweruza 19:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu mwini nyumba anawaturukira nanena nao, lai, abale anga, musacite coipa cotere; popeza mwamuna uyu walowa m'nyumba mwanga, musacite copusa ici.

Oweruza 19

Oweruza 19:16-27