Oweruza 19:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mkazi wace wamng'ono anacita cigololo akali naye, namcokera kumka ku nyumba ya atate wace ku Betelehemu-Yuda, nakhalako nthawi ya miyezi inai.

Oweruza 19

Oweruza 19:1-10