Oweruza 18:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iwo, Taukani, tiwakwerere; pakuti tapenya dziko, ndipo taonani, ndilo lokoma ndithu; ndi inu muli cete kodi? musamacita ulesi kumuka ndi kulowa kulandira dzikolo,

Oweruza 18

Oweruza 18:1-18