Oweruza 18:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pokhala iwo m'nyumba ya Mika, anazindikira mau a mnyamata Mleviyo, napambukirako, nanena naye, Anadza nawe kuno ndani? ucitanji muno? ukhala naco ciani kuno?

Oweruza 18

Oweruza 18:1-8