Oweruza 18:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapfuula kwa ana a Dani. Naceuka iwo nati kwa Mika, Cakusowa ciani, kuti wamemeza anthu ako?

Oweruza 18

Oweruza 18:22-25