Oweruza 18:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo amuna mazana asanu ndi limodzi, omangira zida za nkhondo m'cuuno, anaphumulako a banja la a Dani, anacokera ku Zora, ndi ku Esitaoli.

Oweruza 18

Oweruza 18:1-19