Oweruza 17:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mika ananena naye, Ufumira kuti? Nati kwa iye, Ndine Mlevi wa ku Betelehemu-Yuda, ndirikumuka kugonera kumene ndikapeza pokhala.

Oweruza 17

Oweruza 17:1-13