Oweruza 17:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anambwezera mai wace ndaramazo, mai wace anatapako ndarama mazana awiri, nazipereka kwa woyenga, ndiye anazipanga fane losema ndi fano loyenga; ndipo linakhala m'nyumba ya Mika.

Oweruza 17

Oweruza 17:1-6