Pamenepo Delila anati kwa Samsoni, Ndikupempha, undiuze umo mucokera mphamvu yako yaikuru, ndi cimene angakumange naco, kuti akuzunze.