Oweruza 16:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Samsoni, Ndife nao Afilisti; nadziweramira mwamphamvu; ndipo nyumba idagwa pa akalonga, ndi pa anthu onse anali m'mwemo. Motero akufa amene anawapha pa kufa kwace anaposa amene anawapha akali moyo.

Oweruza 16

Oweruza 16:20-31