Oweruza 16:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati, Afilisti akugwera, Samsoni. Nagalamuka iye m'tulo tace, nati, Ndizituruka ngati nthawi zina, ndi kudzitakasika. Koma sanadziwa kuti Yehova adamcokera.

Oweruza 16

Oweruza 16:19-24