Oweruza 15:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali atapita masiku, nyengo ya kuceka tirigu Samsoni anakaceza ndi mkazi wace ndi kumtengera mbuzi, nati, Ndidzalowa kwa mkazi wanga kucipinda. Koma atate wace sanamlola kulowamo.

Oweruza 15

Oweruza 15:1-8