Oweruza 14:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analira pamaso pace masiku asanu ndi awiriwo pocitika madyerero ao; koma kunali kuti tsiku lacisanu ndi ciwiri anamuuza, popeza anamuumiriza; ndipo anatanthauzira anthu a mtundu wace mwambiwo.

Oweruza 14

Oweruza 14:10-20