Oweruza 13:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mkazi wace ananena naye, Yehova akadafuna kutipha, sakadalandira nsembe yopsereza ndi nsembe yaufa pa dzanja lathu, kapena kutionetsa izi zonse, kapena kutimvetsa zoterezi nthawi yino.

Oweruza 13

Oweruza 13:19-25