Oweruza 12:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anali nao ana amuna makumi atatu; ndi ana akazi makumi atatu anawakwatitsa kwina, natengera ana ace amuna ana akazi makumi atatu ocokera kwina. Ndipo anaweruza Israyeli zaka zisanu ndi ziwiri.

Oweruza 12

Oweruza 12:5-12