Oweruza 12:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo anati kwa iye, Unene tsono Shiboleti; ndipo akati, Siboleti, osakhoza kuchula bwino, amgwira namupha padooko pomwe pa Yordano; ndipo anagwa a Efraimu nthawi ija, zikwi makumi anai mphambu ziwiri.

Oweruza 12

Oweruza 12:5-8