Oweruza 12:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anali nao ana amuna makumi anai ndi zidzukulu zazimuna makumi atatu, akuyenda okwera pa ana a aburu makumi asanu ndi awiri; naweruza Israyeli zaka zisanu ndi zitatu.

Oweruza 12

Oweruza 12:4-15